SomBeat.com
Tandiuze
In(Intro) Charlie again. AK movie on. ( First ves) Mwana kazi tandiuze.! Kodi ndipati pomwe ndimakuphonya? Komaine ndimakuchengetela!!!! Kukwiya km osakutsonya! Ndikungofuna ndikhale ndiiwe basi???. (Hook.) Tandiuze bbeiii ndiziweko zantima mwako. Tandiuze bbeiii ndiziweko zantima mwako!!
Share Direct Link
[Verse 1] Mwana kazi tandiuze Kodi ndipati pomwe ndimakuphonya? Komaine ndimakuchengetela Kukwiya km osakutsonya Ndikungofuna ndikhale ndiiwe basi Palibe wina anga kufanana nawe [Chorus] Tandiuze bbeiii, ndiziweko zantima mwako Tandiuze bbeiii, ndiziweko zantima mwako Ngati moon wakesa mfawanthu Mfawanthu xanderi monga eeeh [Verse 2] Tikwela pamwamba ndi imva Mundee mgona ... ya ma orana maalewa Aliyense akufuna kukhala mbali yathu Tikhale imodzi ine nawe koma Musuke mofewa pazipita bwino Tikaye naye pamwamba pomwepo [Chorus] Tandiuze bbeiii, ndiziweko zantima mwako Tandiuze bbeiii, ndiziweko zantima mwako Ngati moon wakesa mfawanthu Mfawanthu xanderi monga eeeh [Bridge] Ooh, ndikukuwona ndithu Pamene uli pamwiya Zomwe timamufuna zonse Ngati dzuwa lomwe limayaka [Chorus] Tandiuze bbeiii, ndiziweko zantima mwako Tandiuze bbeiii, ndiziweko zantima mwako Ngati moon wakesa mfawanthu Mfawanthu xanderi monga eeeh
Download Music and Video
Sign up now and you will be able to download MP3 videos and music!